Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:4 - Buku Lopatulika

4 Akampatsa mkazi mbuye wake, ndipo akambalira ana aamuna ndi aakazi, mkaziyo ndi ana ake azikhala a mbuye wake, ndipo azituluka ali yekha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Akampatsa mkazi mbuye wake, ndipo akambalira ana aamuna ndi aakazi, mkaziyo ndi ana ake azikhala a mbuye wake, ndipo azituluka ali yekha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ngati mbuyake adampatsa mkazi, ndipo adamubalirapo ana aamuna kapena aakazi, mkaziyo pamodzi ndi anawo onse ndi a mbuyakeyo. Tsono mwamuna yekhayo ndiye adzachoke.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ngati bwana wake amupatsa mkazi ndipo mkaziyo anabereka ana aamuna kapena aakazi, mkazi ndi anawo adzakhala a bwanayo ndipo mwamuna yekhayo ndiye adzamasulidwe.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:4
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Sarai anati kwa Abramu, Taonanitu, Yehova anandiletsa ine kuti ndisabale: lowanitu kwa mdzakazi wanga; kapena ndikalandire ndi iye ana. Ndipo Abramu anamvera mau a Sarai.


Azidulidwatu amene abadwa m'nyumba mwako ndi amene agulidwa ndi ndalama zako: ndipo pangano langa lidzakhala m'thupi mwako pangano losatha.


Akalowa ali yekha azituluka ali yekha; akakhala ndi mkazi, mkazi wake azituluka naye.


Koma mnyamatayo akanenetsa, Ndikonda mbuye wanga, mkazi wanga, ndi ana anga; sindituluka waufulu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa