Eksodo 21:3 - Buku Lopatulika3 Akalowa ali yekha azituluka ali yekha; akakhala ndi mkazi, mkazi wake azituluka naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Akalowa ali yekha azituluka ali yekha; akakhala ndi mkazi, mkazi wake azituluka naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Akakhala kuti anali yekha, adzachokanso yekha. Koma ngati anali ndi mkazi pobwerapo, mkazi wakeyo adzapita naye limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ngati anabwera yekha, amasulidwenso yekha. Koma ngati anali ndi mkazi pamene ankabwera, mkaziyo apite nayenso. Onani mutuwo |