Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ngati anabwera yekha, amasulidwenso yekha. Koma ngati anali ndi mkazi pamene ankabwera, mkaziyo apite nayenso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 Akalowa ali yekha azituluka ali yekha; akakhala ndi mkazi, mkazi wake azituluka naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Akalowa ali yekha azituluka ali yekha; akakhala ndi mkazi, mkazi wake azituluka naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Akakhala kuti anali yekha, adzachokanso yekha. Koma ngati anali ndi mkazi pobwerapo, mkazi wakeyo adzapita naye limodzi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:3
5 Mawu Ofanana  

“Mukagula kapolo wa Chihebri, azikugwirirani ntchito zaka zisanu ndi chimodzi. Koma mʼchaka cha chisanu ndi chiwiri muzimumasula, ndipo asalipire kanthu.


Ngati bwana wake amupatsa mkazi ndipo mkaziyo anabereka ana aamuna kapena aakazi, mkazi ndi anawo adzakhala a bwanayo ndipo mwamuna yekhayo ndiye adzamasulidwe.


“Ngati munthu agulitsa mwana wake wamkazi kukhala mdzakazi, mwanayo asamasulidwe monga achitira ndi akapolo aamuna.


Kenaka iye ndi ana ake achoke, ndipo apite ku fuko lake ndi kubwerera ku malo a makolo ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa