Eksodo 21:35 - Buku Lopatulika35 Ng'ombe ya mwini ikapweteka ng'ombe ya mnzake, nifa, azigulitsa ng'ombe yamoyoyo, nagawe ndalama zake; naigawe, ndi yakufa yomweyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ng'ombe ya mwini ikapweteka ng'ombe ya mnzake, nifa, azigulitsa ng'ombe yamoyoyo, nagawe ndalama zake; naigawe, ndi yakufa yomweyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 “Ng'ombe ya munthu wina ikapha ng'ombe ya mnzake, anthu aŵiriwo agulitse ng'ombe yamoyoyo, ndipo ndalama zake agaŵane. Nyama yake ya ng'ombe yakufayo agaŵanenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 “Ngati ngʼombe ya munthu wina ipha ngʼombe ya mnzake, ngʼombe yamoyo ija igulitsidwe ndipo anthu awiriwo agawane pakati ndalama yake. Achite chimodzimodzi ndi ngʼombe yakufa ija. Onani mutuwo |