Eksodo 21:34 - Buku Lopatulika34 mwini dzenje azilipa; azilipa ndalama kwa mwini nyamayo, koma yakufayo ndi yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 mwini dzenje azilipa; azilipa ndalama kwa mwini nyamayo, koma yakufayo ndi yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 ayenera kulipira chifukwa cha choŵetacho. Alipire ndalama kwa mwini choŵetacho, koma nyamayo atenge ikhale yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 mwini dzenjelo amulipire mwini chiweto chakufacho koma iye atenge chiwetocho. Onani mutuwo |