Eksodo 21:33 - Buku Lopatulika33 Munthu akafukula dzenje, kapena akakumba dzenje, osalivundikira, ndipo ikagwamo ng'ombe kapena bulu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Munthu akafukula dzenje, kapena akakumba dzenje, osalivundikira, ndipo ikagwamo ng'ombe kapena bulu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 “Munthu akasiya dzenje lapululu, kapena akakumba dzenje, koma osaphimbira, tsono ng'ombe kapena bulu nkugweramo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Munthu akasiya dzenje lapululu kapena akakumba dzenje koma wosaphimbapo, ndipo ngʼombe kapena bulu nʼkugweramo, Onani mutuwo |