Eksodo 21:21 - Buku Lopatulika21 Koma akakhala wosafa tsiku limodzi kapena awiri, asalangike, pakuti ndiye ndalama ya mbuye wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma akakhala wosafa tsiku limodzi kapena awiri, asalirike, pakuti ndiye ndalama ya mbuye wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma kapoloyo akakhala moyo tsiku lathunthu kapena masiku aŵiri, mbuyakeyo asalangidwe. Kapoloyo ndi chuma cha mbuyakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma ngati kapolo uja akhala ndi moyo tsiku lonse kapena masiku awiri, ndiye kuti mbuye uja asalangidwe chifukwa kapolo ndi chuma chake. Onani mutuwo |