Eksodo 21:19 - Buku Lopatulika19 akaukanso, nakayendayenda pabwalo ndi ndodo yake, womkanthayo azikhala womasuka; pakutsotsa pake pokha azimbwezera, namchizitse konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 akaukanso, nakayendayenda pabwalo ndi ndodo yake, womkanthayo azikhala womasuka; pakutsotsa pake pokha azimbwezera, namchizitse konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 koma pambuyo pake adzuka nkumayendayenda kunja, ngakhale kuti akuyenda ndi ndodo, munthu amene adammenyayo sadzalangidwa molipsira, koma adzangolipira chifukwa cha nthaŵi yotayika pa bedi ija. Ndipo adzayenera kumsamala ndithu mnzakeyo mpaka atachira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 kenaka nachira ndi kuyamba kuyenda ndi ndodo kutuluka kunja kwa nyumba yake, ndiye kuti womenya mnzakeyo sadzayimbidwa mlandu. Komabe adzayenera kulipira womenyedwayo chifukwa cha nthawi imene anagona pa bedi ija, ndiponso ayenera kumusala mpaka atachiritsitsa. Onani mutuwo |