Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:18 - Buku Lopatulika

18 Akalimbana amuna, ndipo wina akakantha mnzake ndi mwala, kapena ndi nkhonya, wosafa iye, koma wakhulungira pakama;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Akalimbana amuna, ndipo wina akakantha mnzake ndi mwala, kapena ndi nkhonya, wosafa iye, koma wakhulungira pakama;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 “Anthu akamenyana, ndipo wina mwa iwowo amenya mnzake ndi mwala kapena nkhonya, koma osamupha mnzakeyo, munthu womenyedwayo akadwala nakagona pa bedi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 “Ngati anthu awiri akangana ndipo wina amenya mnzake ndi mwala kapena nkhonya koma wosamupha, womenyedwayo akadwala nagona pa bedi,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:18
8 Mawu Ofanana  

Ndipo mdzakazi wanu ndinali nao ana aamuna awiri, ndipo awiriwo analimbana kumunda, panalibe wina wakuwaletsa, koma wina anakantha mnzake namupha.


M'mawa mwake anatulukanso, ndipo, taonani, anthu awiri Ahebri alikumenyana; ndipo ananena ndi wochimwayo, kuti, Umpandiranji mnzako?


Munthu wakutemberera atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.


akaukanso, nakayendayenda pabwalo ndi ndodo yake, womkanthayo azikhala womasuka; pakutsotsa pake pokha azimbwezera, namchizitse konse.


Munthu akakantha mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, ndi ndodo, ndipo akafa padzanja pake; ameneyo alangidwe ndithu.


Akayambana amuna, nakakantha mkazi ali ndi pakati, kotero kuti abala, koma alibe kuphwetekwa; alipe ndithu, monga momwe amtchulira mwamuna wa mkaziyo; apereke monga anena oweruza.


Akalimbana wina ndi mnzake, nakayandikiza mkazi wa winayo kulanditsa mwamuna wake m'dzanja la wompandayo, nakatulutsa dzanja lake, ndi kumgwira kudzivalo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa