Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:17 - Buku Lopatulika

17 Munthu wakutemberera atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Munthu wakutemberera atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 “Munthu aliyense wotemberera bambo wake kapena mai wake, aphedwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 “Aliyense amene atemberera abambo ake kapena amayi ake ayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:17
11 Mawu Ofanana  

Uzilemekeza atate wako ndi amai ako; kuti achuluke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.


Akalimbana amuna, ndipo wina akakantha mnzake ndi mwala, kapena ndi nkhonya, wosafa iye, koma wakhulungira pakama;


Wotemberera atate wake ndi amake, nyali yake idzazima mu mdima woti bii.


Pali mbadwo wotemberera atate ao, osadalitsa amai ao.


Diso lochitira atate wake chiphwete, ndi kunyoza kumvera amake, makwangwala a kumtsinje adzalikolowola, ana a mphungu adzalidya.


Munthu akakhala naye mwana wamwamuna wopulukira, ndi wopikisana naye, wosamvera mau a atate wake, kapena mau a mai wake, wosawamvera angakhale anamlanga;


Pamenepo amuna onse a mzinda wake amponye miyala kuti afe; chotero muchotse choipacho pakati panu; ndipo Israele wonse adzamva, nadzaopa.


Wotembereredwa iye wakupeputsa atate wake kapena mai wake. Ndi anthu onse anene, Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa