Eksodo 21:16 - Buku Lopatulika16 Iye wakuba munthu, angakhale wamgulitsa, kapena akampeza m'dzanja lake, aphedwe ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Iye wakuba munthu, angakhale wamgulitsa, kapena akampeza m'dzanja lake, aphedwe ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Munthu aliyense amene aba munthu mnzake ndi kumgulitsa kapena kungomsunga ngati kapolo, aphedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Munthu aliyense amene aba munthu mnzake, ndi kukamugulitsa, kapena kumangomusunga, ayenera kuphedwa. Onani mutuwo |
malonda a golide, ndi a siliva, ndi a mwala wa mtengo wake, ndi a ngale, ndi a nsalu yabafuta, ndi a chibakuwa, ndi a yonyezimira, ndi a mlangali; ndi mitengo yonse ya fungo lokoma, ndi chotengera chilichonse cha minyanga ya njovu, ndi chotengera chilichonse chamtengo wa mtengo wake wapatali, ndi chamkuwa ndi chachitsulo, ndi chansangalabwi;