Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:15 - Buku Lopatulika

15 Munthu wakukantha atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Munthu wakukantha atate wake, kapena amai wake, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 “Munthu aliyense amene amenya bambo wake kapena mai wake, aphedwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 “Munthu aliyense amene amenya abambo ake kapena mayi ake ayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:15
7 Mawu Ofanana  

Koma munthu akachita dala pa mnzake, kumupha monyenga; uzimchotsa ku guwa langa la nsembe, kuti afe.


Iye wakuba munthu, angakhale wamgulitsa, kapena akampeza m'dzanja lake, aphedwe ndithu.


Pali mbadwo wotemberera atate ao, osadalitsa amai ao.


Diso lochitira atate wake chiphwete, ndi kunyoza kumvera amake, makwangwala a kumtsinje adzalikolowola, ana a mphungu adzalidya.


Wotembereredwa iye wakukantha mnansi wake m'tseri. Ndi anthu onse anene, Amen.


podziwa ichi, kuti lamulo siliikika kwa munthu wolungama, koma kwa osaweruzika ndi osamvera lamulo, osapembedza, ndi ochimwa, osalemekeza ndi amnyozo, akupha atate ndi akupha amai, akupha anzao,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa