Eksodo 21:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Akapanda kumchitira zimenezi, ammasule kuti akhale mfulu, koma osalandirapo ndalama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma ngati sangathe kumuchitira zonsezi, ndiye amuleke apite popanda kulipira kanthu. Onani mutuwo |