Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 21:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Koma ngati sangathe kumuchitira zonsezi, ndiye amuleke apite popanda kulipira kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Akapanda kumchitira zimenezi, ammasule kuti akhale mfulu, koma osalandirapo ndalama.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:11
2 Mawu Ofanana  

Ngati akwatira mkazi wina, asamumane woyambayo chakudya ngakhale chovala ndipo apiritirize kugona naye ngati mkazi wake.


“Munthu aliyense amene amenya mnzake namupha, iyenso ayenera kuphedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa