Eksodo 20:12 - Buku Lopatulika12 Uzilemekeza atate wako ndi amai ako; kuti achuluke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Uzilemekeza atate wako ndi amai ako; kuti achuluke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 “Uzilemekeza atate ndi amai ako, kuti masiku a moyo wako achuluke m'dziko limene Chauta, Mulungu wako, akukupatsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Lemekeza abambo ako ndi amayi ako kuti ukhale ndi moyo wautali mʼdziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa. Onani mutuwo |