Eksodo 2:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anaona mwana, ndi Mose anamutcha dzina lake Geresomo; pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko la eni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anaona mwana, ndi Mose anamutcha dzina lake Geresomo; pakuti anati, Ndakhala mlendo m'dziko la eni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Zipora adabala mwana wamwamuna. Pamenepo Mose adati, “Ndine mlendo m'dziko lachilendo.” Motero adamutcha mwanayo Geresomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Zipora anabereka mwana wa mwamuna amene Mose anamutcha Geresomu, popeza anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko la eni.” Onani mutuwo |