Eksodo 19:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Mose anadza, naitana akulu a anthu, nawaikira pamaso pao mau awa onse amene Yehova adamuuza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Mose anadza, naitana akulu a anthu, nawaikira pamaso pao mau awa onse amene Yehova adamuuza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamenepo Mose adakaitana atsogoleri a Aisraele, ndipo adaŵauza zonse zimene Chauta adamlamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo Mose anabwerera ndi kuyitanitsa akuluakulu. Atabwera anawafotokozera mawu amene Yehova anamulamulira kuti adzanene. Onani mutuwo |