Eksodo 19:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo Mose anati kwa Yehova, Anthu sangathe kukwera m'phiri la Sinai; pakuti Inu mwatichenjeza, ndi kuti, Lemba malire m'phirimo, ndi kulipatula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo Mose anati kwa Yehova, Anthu sangathe kukwera m'phiri la Sinai; pakuti Inu mwatichenjeza, ndi kuti, Lemba malire m'phirimo, ndi kulipatula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Mose adayankha Chauta kuti, “Anthuwo sangakwere ai, chifukwa mudachenjezeratu kuti, ‘Mulembe malire kuzungulira phirilo, ndipo mulipatule kuti likhale loyera.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Mose anati kwa Yehova, “Anthu sangakwere phiri la Sinai chifukwa inu munatichenjeza. Lembani malire kuzungulira phiri ndipo mulipatule kuti likhale loyera.” Onani mutuwo |