Eksodo 19:22 - Buku Lopatulika22 Ansembenso, akuyandikiza kwa Yehova adzipatulitse, angawapasule Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ansembenso, akuyandikiza kwa Yehova adzipatulitse, angawapasule Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ngakhale ansembe amene akufika pafupi ndi Ine adziyeretse, kuti ndingadzaŵalange.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ngakhale ansembe amene amatumikira pamaso pa Yehova ayenera kudziyeretsa kuopa kuti ndingadzawalange.” Onani mutuwo |