Eksodo 19:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tsika, chenjeza anthu, kuti angapyolere kwa Yehova kudzaona, ndipo angagwe ambiri a iwowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tsika, chenjeza anthu, kuti angapyolere kwa Yehova kudzaona, ndipo angagwe ambiri a iwowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chauta adauza Mose kuti, “Tsika pansi, ndipo uza anthu kuti asapitirire malire ndi kubwera kumadzayang'ana kwa Ine, kuti ambiri mwa iwowo angadzafe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 ndipo Yehova anati kwa iye, “Tsika ukawachenjeze anthu kuti asayesere kudutsa malire kuti adzandione chifukwa ambiri a iwo adzafa. Onani mutuwo |