Eksodo 19:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamutu pake paphiri; ndipo Yehova anaitana Mose akwere pamutu paphiri; ndi Mose anakwerapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Yehova anatsikira pa phiri la Sinai, pamutu pake pa phiri; ndipo Yehova anaitana Mose akwere pamutu pa phiri; ndi Mose anakwerapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Chauta adafika pamwamba pa phiri la Sinai, adaitana Mose pamwamba pa phiri, ndipo Moseyo adakwera phirilo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Yehova anatsika nafika pamwamba pa phiri la Sinai, ndipo anayitana Mose kuti apite pa phiripo. Choncho Mose anakwera, Onani mutuwo |