Eksodo 19:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo pamene liu la lipenga linamveka linakulirakulira, Mose ananena, ndi Mulungu anamyankha ndi mau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo pamene liu la lipenga linamveka linakulirakulira, Mose ananena, ndi Mulungu anamyankha ndi mau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Liwu la mbetete linkakulirakulira. Apo Mose adalankhula, ndipo Mulungu adamuyankha ndi mabingu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Liwu la lipenga linkakulirakulira. Tsono Mose anayankhula ndipo Yehova anamuyankha ndi mabingu. Onani mutuwo |