Eksodo 19:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti anachoka ku Refidimu, nalowa m'chipululu cha Sinai, namanga tsasa m'chipululumo; ndipo Israele anamanga tsasa pamenepo pandunji paphirilo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti anachoka ku Refidimu, nalowa m'chipululu cha Sinai, namanga tsasa m'chipululumo; ndipo Israele anamanga tsasa pamenepo pandunji pa phirilo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Atachoka ku Refidimu adakafika ku chipululu cha Sinai, kumene adamangako mahema pafupi ndi phirilo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Atachoka ku Refidimu, anafika ku Sinai, ndipo Aisraeli anamangako misasa yawo moyangʼanana ndi phirilo. Onani mutuwo |