Eksodo 19:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Atachoka ku Refidimu, anafika ku Sinai, ndipo Aisraeli anamangako misasa yawo moyangʼanana ndi phirilo. Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Pakuti anachoka ku Refidimu, nalowa m'chipululu cha Sinai, namanga tsasa m'chipululumo; ndipo Israele anamanga tsasa pamenepo pandunji paphirilo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti anachoka ku Refidimu, nalowa m'chipululu cha Sinai, namanga tsasa m'chipululumo; ndipo Israele anamanga tsasa pamenepo pandunji pa phirilo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Atachoka ku Refidimu adakafika ku chipululu cha Sinai, kumene adamangako mahema pafupi ndi phirilo. Onani mutuwo |