Eksodo 19:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anati kwa anthu, Mukonzekeretu tsiku lachitatu nimusayandikiza mkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anati kwa anthu, Mukonzekeretu tsiku lachitatu nimusayandikiza mkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Kenaka Mose adaŵauza kuti, “Mkucha uno, mukonzeke. Musayandikize mkazi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kenaka iye anati kwa anthu, “Konzekerani tsiku lachitatu, musagone pamodzi ndi mkazi.” Onani mutuwo |