Eksodo 19:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Mose anatsika m'phiri kunka kwa anthu, nawapatulitsa anthu; natsuka iwo zovala zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Mose anatsika m'phiri kunka kwa anthu, nawapatulitsa anthu; natsuka iwo zovala zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Mose adatsika phiri, nakafika kwa anthuwo, ndipo adaŵayeretsa. Anthuwo adachapadi zovala zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsono Mose anatsika phiri lija nafika kwa anthu aja ndi kuwayeretsa. Iwo anachapa zovala zawo. Onani mutuwo |