Eksodo 18:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yetero anakondwera chifukwa cha zabwino zonse Yehova adazichitira Israele, ndi kuwalanditsa m'dzanja la Aejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yetero anakondwera chifukwa cha zabwino zonse Yehova adazichitira Israele, ndi kuwalanditsa m'dzanja la Aejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yetero adakondwa kwambiri ndi ntchito zabwino zimene Chauta adaachitira Aisraele pakuŵapulumutsa kwa Aejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yetero anakondwa kwambiri atamva zabwino zonse zimene Yehova anachitira Aisraeli powapulumutsa mʼdzanja la Aigupto. Onani mutuwo |