Eksodo 18:23 - Buku Lopatulika23 Ukachite chinthuchi, ndi Mulungu akakuuza chotero, udzakhoza kupirira, ndi anthu awa onse adzapita kwao mumtendere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ukachite chinthuchi, ndi Mulungu akakuuza chotero, udzakhoza kupirira, ndi anthu awa onse adzapita kwao mumtendere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Mukachita zimenezi monga Mulungu akulamulira, simudzafooka, ndipo anthu onseŵa adzatha kumabwerera kwao, zao zonse zitakonzeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ngati mutsatira malangizowa monga mmene Mulungu wakulamulirani ndiye kuti simudzafowoka ndipo anthu onsewa adzapita kwawo mu mtendere.” Onani mutuwo |