Eksodo 16:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo ana a Israele anatero, naola wina wambiri, wina pang'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo ana a Israele anatero, naola wina wambiri, wina pang'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Aisraele adachitadi zimenezo. Ena adatola tambiri, koma ena pang'ono. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Aisraeli anachita zonse anawawuza. Ena anatola zambiri ena zochepa. Onani mutuwo |