Eksodo 16:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo kunali madzulo zinakwera zinziri, ndipo zinakuta tsasa, ndi m'mawa padagwa mame pozungulira tsasa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo kunali madzulo zinakwera zinziri, ndipo zinakuta tsasa, ndi m'mawa padagwa mame pozungulira tsasa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Motero madzulo kudagwa zinziri, ndipo zidadzaza ponseponse pamahemapo. M'maŵa ndithu padagwa mame ponse pozungulira mahemawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Madzulo amenewo panatuluka zinziri zimene zinali ponseponse pa misasa yawo, ndipo mmawa panali mame kuzungulira misasa yawo. Onani mutuwo |