Eksodo 15:4 - Buku Lopatulika4 Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira mu Nyanja Yofiira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira m'Nyanja Yofiira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Chauta adaponya m'nyanja magaleta a Farao pamodzi ndi gulu lake lankhondo, adammizira atsogoleri ake amphamvu m'Nyanja Yofiira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Magaleta a Farao ndi asilikali ake ankhondo Iye wawaponya mʼnyanja. Akatswiri ankhondo amphamvu a Farao amizidwa mʼNyanja Yofiira. Onani mutuwo |