Eksodo 15:15 - Buku Lopatulika15 Pamenepo mafumu a Edomu anadabwa; agwidwa nako kunthunthumira amphamvu a ku Mowabu; okhala mu Kanani onse asungunuka mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pamenepo mafumu a Edomu anadabwa; agwidwa nako kunthunthumira amphamvu a ku Mowabu; okhala m'Kanani onse asungunuka mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsopano lino mafumu a ku Edomu ataya mtima. Atsogoleri a ku Mowabu ayambapo kunjenjemera. Onse a ku Kanani agooka m'nkhongono. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Tsopano mafumu a ku Edomu agwidwa ndi mantha aakulu, otsogolera a dziko la Mowabu akunjenjemera ndi mantha, ndipo anthu a ku Kanaani asungunuka ndi mantha. Onani mutuwo |