Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 15:12 - Buku Lopatulika

12 Mwatambasula dzanja lanu lamanja, nthaka inawameza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mwatambasula dzanja lanu lamanja, nthaka inawameza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Mudatambalitsa dzanja lanu lamanja, ndipo nthaka idaŵameza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Munatambasula dzanja lanu lamanja ndipo dziko linawameza.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 15:12
3 Mawu Ofanana  

Ndingakhale ndiyenda pakati pa nsautso, mudzandipatsa moyo; mudzatambasula dzanja lanu pa mkwiyo wa adani anu, ndipo dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.


Dzanja lanu lamanja, Yehova, lalemekezedwa ndi mphamvu, dzanja lanu lamanja, Yehova, laphwanya mdani.


Umenewu ndi uphungu wopangira dziko lonse; ndipo ili ndi dzanja lotambasulidwa pa amitundu onse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa