Eksodo 15:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Munatambasula dzanja lanu lamanja ndipo dziko linawameza. Onani mutuwoBuku Lopatulika12 Mwatambasula dzanja lanu lamanja, nthaka inawameza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Mwatambasula dzanja lanu lamanja, nthaka inawameza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mudatambalitsa dzanja lanu lamanja, ndipo nthaka idaŵameza. Onani mutuwo |