Eksodo 14:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anamanga galeta lake, napita nao anthu ake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anamanga galeta lake, napita nao anthu ake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pamenepo Farao adakonzetsa galeta lake lankhondo, ndipo adauza asilikali ake kuti apite naye limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho anakonzetsa galeta lake ndipo ananyamuka pamodzi ndi ankhondo ake. Onani mutuwo |