Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 14:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Choncho anakonzetsa galeta lake ndipo ananyamuka pamodzi ndi ankhondo ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Ndipo anamanga galeta lake, napita nao anthu ake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo anamanga galeta lake, napita nao anthu ake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Pamenepo Farao adakonzetsa galeta lake lankhondo, ndipo adauza asilikali ake kuti apite naye limodzi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 14:6
3 Mawu Ofanana  

Farao, mfumu ya Igupto atamva kuti anthu aja athawa, iye pamodzi ndi nduna zake anasintha maganizo awo pa Israeli ndipo anati, “Ife tachita chiyani? Tawalola Aisraeli kuti apite ndi kuleka kutitumikira?”


Iye anatenga magaleta 600 abwino kwambiri pamodzi ndi magaleta ena a dziko la Igupto. Anatenganso akuluakulu onse ankhondo.


Magaleta a Farao ndi asilikali ake ankhondo Iye wawaponya mʼnyanja. Akatswiri ankhondo amphamvu a Farao amizidwa mʼNyanja Yofiira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa