Eksodo 14:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ufuuliranji kwa Ine? Lankhula ndi ana a Israele kuti aziyenda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ufuuliranji kwa Ine? Lankhula ndi ana a Israele kuti aziyenda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo Chauta adafunsa Mose kuti, “Chifukwa chiyani ukulira kwa ine? Auze Aisraele kuti aziyenda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kenaka Yehova anati kwa Mose, “Chifukwa chiyani ukufuwulira kwa ine? Uwuze Aisraeli aziyenda. Onani mutuwo |