Eksodo 14:14 - Buku Lopatulika14 Yehova adzakugwirirani nkhondo, ndipo inu mudzakhala chete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Yehova adzakugwirirani nkhondo, ndipo inu mudzakhala chete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Chauta ndiye amene akumenyereni nkhondo. Inuyo simuchitapo kanthu konse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Yehova adzakumenyerani nkhondo. Inu mungokhala chete.” Onani mutuwo |