Eksodo 13:13 - Buku Lopatulika13 Koma woyamba yense wa bulu uzimuombola ndi mwanawankhosa; ndipo ukapanda kumuombola uzimthyola khosi; koma oyamba onse a munthu mwa ana ako uziwaombola. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma woyamba yense wa bulu uzimuombola ndi mwanawankhosa; ndipo ukapanda kumuombola uzimthyola khosi; koma oyamba onse a munthu mwa ana ako uziwaombola. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Koma mwanawabulu woyamba kubadwa, muzimuwombolanso pakupereka mwanawankhosa m'malo mwake. Ngati simufuna kumuwombola, muzimthyola khosi. Muziwombola mwana wamwamuna wachisamba aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Koma mwana woyamba kubadwa wa bulu muzikamuwombola ndi mwana wankhosa, koma ngati simukamuwombola, muzikamuthyola khosi. Mwana wamwamuna woyamba kubadwa muzikamuwombola. Onani mutuwo |