Eksodo 12:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo mukhale naye chisungire kufikira tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi womwe; ndipo gulu lonse la Israele lizamuphe madzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo mukhale naye chisungire kufikira tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi womwe; ndipo bungwe lonse la anthu a Israele lizimupha madzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mumsunge mpaka tsiku la 14 la mwezi, pamene khamu lonse la Aisraele lidzaphe nyama zaozo madzulo ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Muzisunge mpaka tsiku la khumi ndi chinayi la mwezi, pamene gulu lonse la Aisraeli lidzaphe nyamazo madzulo. Onani mutuwo |