Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 12:40 - Buku Lopatulika

40 Ndipo kukhala kwa ana a Israele anakhala mu Ejipito ndiko zaka mazana anai kudza makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ndipo kukhala kwa ana a Israele anakhala m'Ejipito ndiko zaka mazana anai kudza makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Aisraele adakhalako zaka 430 ku Ejipito kuja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Ndipo Aisraeli anakhala ku Igupto kwa zaka 430.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 12:40
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anati kwa Abramu, Dziwitsa ndithu kuti mbeu zako zidzakhala alendo m'dziko la eni, ndipo zidzatumikira iwo, ndipo iwo adzasautsa izo zaka mazana anai;


Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wachinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.


Tiye tsopano, ndikutuma kwa Farao, kuti utulutse anthu anga, ana a Israele mu Ejipito.


Mulungu wa anthu awa Israele anasankha makolo athu, nakweza anthuwo pakugonerera iwo m'dziko la Ejipito, ndipo ndi dzanja lokwezeka anawatulutsa iwo m'menemo.


Koma Mulungu analankhula chotero, kuti mbeu yake idzakhala alendo m'dziko la eni, ndipo adzawachititsa ukapolo, nadzawachitira choipa, zaka mazana anai.


Ndi chikhulupiriro anakhala mlendo kudziko la lonjezano, losati lake, nakhalira m'mahema pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, olowa nyumba pamodzi ndi iye a lonjezano lomwelo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa