Eksodo 12:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Aejipito anaumiriza anthuwo, nafulumira kuwatulutsa m'dziko; pakuti anati, Tili akufa tonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Aejipito anaumiriza anthuwo, nafulumira kuwatulutsa m'dziko; pakuti anati, Tili akufa tonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Aejipito adafulumizitsa anthu kuti achoke m'dzikomo, namanena kuti, “Tifatu tonsefe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Aigupto anawawumiriza anthuwo kuti atuluke mofulumira ndi kusiya dziko lawo. Iwo anati, “Ngati sitiwalola kutero, tonse tidzafa.” Onani mutuwo |