Eksodo 12:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo kudzakhala, pamene mulowa m'dziko limene Yehova adzakupatsani, monga analankhula, muzisunga kutumikira kumeneku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo kudzakhala, pamene mulowa m'dziko limene Yehova adzakupatsani, monga analankhula, muzisunga kutumikira kumeneku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndipo mukadzaloŵa m'dziko limene Chauta akukupatsanilo, monga momwe adalonjezera, muzidzasunga mwambo umenewu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova adzakupatseni monga analonjeza, mukasunge mwambo umenewu. Onani mutuwo |