Eksodo 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Farao sadzamvera inu; kuti zozizwa zanga zichuluke m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Farao sadzamvera inu; kuti zozizwa zanga zichuluke m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chauta adauza Mose kuti, “Farao sadzakumvera iwe, kuti pakutero, Ine ndichite zozizwitsa m'dziko la Ejipito.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yehova ananena kwa Mose kuti, “Farao adzakana kukumvera, kuti zodabwitsa zanga zichuluke mʼdziko la Igupto.” Onani mutuwo |