Eksodo 10:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anawabwereretsa Mose ndi Aroni kwa Farao, nanena nao, Mukani, katumikireni Yehova Mulungu wanu. Koma amene adzapitawo ndiwo yani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anawabwereretsa Mose ndi Aroni kwa Farao, nanena nao, Mukani, katumikireni Yehova Mulungu wanu. Koma amene adzapitawo ndiwo yani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero Farao adaitananso Mose ndi Aroni naŵauza kuti, “Pitani mukapembedze Chauta, Mulungu wanu. Koma tsono apite ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho Mose ndi Aaroni anayitanidwanso kwa Farao ndipo anati, “Pitani kapembedzeni Yehova Mulungu wanu. Koma ndani amene adzapite?” Onani mutuwo |