Eksodo 10:25 - Buku Lopatulika25 Koma Mose anati, Mutipatsenso m'dzanja mwathu nsembe zophera ndi nsembe zopsereza, kuti timkonzere Yehova Mulungu wathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma Mose anati, Mutipatsenso m'dzanja mwathu nsembe zophera ndi nsembe zopsereza, kuti timkonzere Yehova Mulungu wathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mose adati, “Tsonotu muyenera kutipatsa ndinu zokaperekera nsembe zopsereza kwa Chauta, Mulungu wathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Koma Mose anati, “Ndiye inu mutipatse nsembe zopsereza zoti tikapereke kwa Yehova Mulungu wathu. Onani mutuwo |