Eksodo 1:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo inalowa mfumu yatsopano mu ufumu wa Ejipito, imene siinadziwe Yosefe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo inalowa mfumu yatsopano m'ufumu wa Ejipito, imene siinadziwa Yosefe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pambuyo pake padaloŵa mfumu ina imene sidadziŵe za Yosefe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pambuyo pake mfumu yatsopano imene sinkamudziwa Yosefe, inayamba kulamulira dziko la Igupto. Onani mutuwo |