Eksodo 1:7 - Buku Lopatulika7 Ana a Israele ndipo anaswana, nabalana, nachuluka, nakhala nazo mphamvu zazikulu; ndipo dziko linadzala nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ana a Israele ndipo anaswana, nabalana, nachuluka, nakhala nazo mphamvu zazikulu; ndipo dziko linadzala nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma adzukulu a Aisraele adabala ana ambirimbiri. Adachulukana nakhala amphamvu kwambiri nkudzaza dzikolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma Aisraeli anaberekana ndi kuchuluka kwambiri nakhala amphamvu kwambiri, kotero kuti anadzaza dzikolo. Onani mutuwo |