Eksodo 1:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo amoyo onse amene anatuluka m'chuuno mwake mwa Yakobo ndiwo makumi asanu ndi awiri; koma Yosefe anali mu Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo amoyo onse amene anatuluka m'chuuno mwake mwa Yakobo ndiwo makumi asanu ndi awiri; koma Yosefe anali m'Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chiŵerengero chenicheni cha anthu obadwa mwa Yakobe chinali makumi asanu ndi aŵiri. Yosefe anali atakhazikika kale ku Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu onse obadwa mwa Yakobo analipo 70. Yosefe nʼkuti ali kale ku Igupto. Onani mutuwo |