Eksodo 1:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu onse obadwa mwa Yakobo analipo 70. Yosefe nʼkuti ali kale ku Igupto. Onani mutuwoBuku Lopatulika5 Ndipo amoyo onse amene anatuluka m'chuuno mwake mwa Yakobo ndiwo makumi asanu ndi awiri; koma Yosefe anali mu Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo amoyo onse amene anatuluka m'chuuno mwake mwa Yakobo ndiwo makumi asanu ndi awiri; koma Yosefe anali m'Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chiŵerengero chenicheni cha anthu obadwa mwa Yakobe chinali makumi asanu ndi aŵiri. Yosefe anali atakhazikika kale ku Ejipito. Onani mutuwo |